Pular para o conteúdo
Publicidade

LUKA 17

Za Ufumu wa Mulungu

20 Ndipo Afarisi atamufunsa Iye kuti, ufumu wa Mulungu udzabwera liti, Yesu anayankha kuti, "Mulungu sakhazikitsa ufumu wake mooneka ndi maso, 21 kapenanso kuti anthu adzati, Uwu uli apa,kapena Uwo uli apo,Pakuti taonani ufumu wa Mulungu uli pakati panu."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também