Pular para o conteúdo
Publicidade

Luka 18:1,7,8

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

Fanizo la Mayi Wakhama pa Kupempha

1 Kenaka Yesu anawuza ophunzira ake fanizo kuwaonetsa kuti iwo ayenera kumapemphera nthawi zonse ndikuti asafowoke.

7 Tsono chingamuletse nʼchiyani Mulungu kubweretsa chilungamo kwa osankhika ake, amene amalira kwa Iye usana ndi usiku? Kodi adzapitirirabe osawalabadira? 8 Ine ndikukuwuzani inu, adzaonetsetsa kuti alandire chilungamo, ndiponso mofulumira. Komabe, pamene Mwana wa Munthu akubwera, kodi adzapeza chikhulupiriro pa dziko lapansi?"

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    1 Ndiipo Yesu wadaakambila ochatila chifani ichi kwaalangiza umo afunikila kupembhela popande kulema.

    7 Bwanji, Mnungu siwaathangatila wandhu wasangha yawo ampembha kupunda popande kulema usana ni usiku? Bwanji, siwachedwa kwaapacha? 8 Nikukambilani, kuti siwakupacheni yayo mfuna kwa chisanga. Bwanji, yapo siwafike ine mwana wa mundhu, bwanji sinapheze wandhu ali ni chikkulupi pano pajhiko?"

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.