10 Gulu la anthuwo linafunsa kuti, "Nanga tsono tichite chiyani?"
11 Yohane anayankha kuti, "Munthu amene ali ndi malaya awiri apatseko amene alibe, ndi amene ali ndi chakudya achitenso chimodzimodzi."

+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.