Pular para o conteúdo
Publicidade

LUKA 4

3 Mdierekezi anati kwa Iye, "Ngati ndiwe Mwana wa Mulungu, uza mwala uwu kuti usanduke buledi."

4 Yesu anayankha kuti, "Zalembedwa: Munthu sadzakhala ndi moyo ndi chakudya chokha.’ "

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também