Pular para o conteúdo
Publicidade

LUKA 5

Yesu Achiritsa Munthu Wakhate

12 Yesu ali ku mudzi wina, munthu amene anali ndi khate thupi lonse anabwera kwa Iye. Munthuyo ataona Yesu, anagwa chafufumimba ndipo anamupempha Iye kuti, "Ambuye, ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa."

13 Yesu anatambasula dzanja lake namukhudza munthuyo. Iye anati, "Ine ndikufuna, yeretsedwa!" Ndipo nthawi yomweyo khate lake linachoka.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também