Pular para o conteúdo
Publicidade

Levítico 26

3 " Mukamayenda motsata malangizo anga ndi kumvera mosamalitsa malamulo anga, 4 ndidzakupatsani mvula pa nyengo yake. Nthaka yanu idzabala zokolola zake, ndipo mitengo ya mʼmunda idzabala zipatso zake.

Veja também