Pular para o conteúdo
Publicidade

MARKO 1

Yesu Ayitana Ophunzira ake Oyamba

16 Pamene Yesu ankayenda mʼmbali mwa nyanja ya Galileya, anaona Simoni ndi mʼbale wake Andreya akuponya khoka mʼnyanja, popeza anali asodzi. 17 Yesu anati, "Bwerani, tsateni Ine, ndipo ndidzakusandutsani asodzi a anthu." 18 Nthawi yomweyo anasiya makoka awo namutsata Iye.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também