Pular para o conteúdo
Publicidade

Marcos 1

Kubatizidwa ndi Kuyesedwa kwa Yesu

9 Pa nthawi imeneyo Yesu anabwera kuchokera ku Nazareti wa ku Galileya ndipo anabatizidwa ndi Yohane mu mtsinje wa Yorodani. 11 Ndipo Mawu anamveka kuchokera kumwamba: "Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa; ndipo ndikondwera nawe."

Veja também