Pular para o conteúdo
Publicidade

Marcos 11

Yesu Atemberera Mkuyu

12 Mmawa mwake pamene amachoka ku Betaniya, Yesu anamva njala. 13 Ataonera patali mtengo wamkuyu uli ndi masamba, anapita kuti akaone ngati unali ndi chipatso chilichonse. Atafika, sanapezemo kanthu koma masamba, chifukwa sinali nthawi ya nkhuyu. 14 Ndipo Iye anati kwa mtengo, "Palibe amene adzadyenso chipatso kuchokera kwa iwe." Ndipo ophunzira ake anamva Iye akunena izi.

Veja também