22 Yesu anayankha kuti, "Khalani ndi chikhulupiriro mwa Mulungu. 23 Zoonadi, Ine ndikuwuzani kuti ngati wina aliyense angalamule phiri ili kuti, ‘Pita, kadziponye mʼnyanja,’ ndipo wosakayika mu mtima mwake koma kukhulupirira kuti chimene akunena chidzachitika, chidzachitikadi kwa iyeyo. 24 Nʼchifukwa chake ndikukuwuzani kuti chilichonse chimene mupempha mʼpemphero, khulupirirani kuti mwalandira, ndipo chidzakhala chanu. 25 Pamene muyimirira kupemphera, ngati muli ndi chifukwa ndi wina, mukhululukireni, kuti Atate anu akumwamba akukhululukireni machimo anu."
Publicidade
Marko 11:22-25
TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
Em outras traduções
- NTNYBL2025 Nyanja
22 Yesu wadamkambila, "Mkhulupilileni Mnungu. 23 Nikukambilani uzene, mundhu waliyonjhe wakalikambila phili ili kuti lipite likajivyale mnyanja ya mchele, popande kukhaikila mumtima mwake, nambho wakakhulupilia kuti chindhu icho wachikamba sichichokele, ni Mnungu siwamchitile. 24 Chipano nikukambilani, yapo msali ni kupembha chindhu, khulupililani kuti mwachilandila, nianyiimwe simchipate. 25 Ni yapo mpembhela, mlekelelane, kila mundhu wamlekelele mnjake uyo wamlakwila, ni Atate wanu ali kumwamba siakulekeleleni anyiimwe volakwa vanu.
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.