Pular para o conteúdo
Publicidade

Marcos 12

30 Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse, ndi moyo wako wonse, ndi nzeru zako zonse ndi mphamvu zako zonse. 31 Lachiwiri ndi ili: Konda mnansi wako monga iwe mwini.Palibe lamulo lina loposa amenewa."

Veja também