Pular para o conteúdo
Publicidade

Marko 12:41-44

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

Chopereka cha Mayi Wamasiye

41 Yesu anakhala pansi moyangʼanana ndi pamene amaperekera zopereka ndipo amaona anthu akupereka ndalama zawo mʼthumba la Nyumba ya Mulungu. Anthu ambiri olemera anaponya ndalama zambiri. 42 Koma mkazi wamasiye, wosauka anabwera ndi kuyikamo tindalama tiwiri ta kopala, tongokwanira theka la ndalama.

43 Yesu anayitana ophunzira ake nati, "Zoonadi, ndikuwuzani kuti mayi wosauka wamasiyeyu waponya zambiri mʼthumbali kuposa ena onsewa. 44 Iwo apereka molingana ndi chuma chawo; koma iye, mwaumphawi wake, wapereka zonse anali nazo ngakhale zoti akanagulira chakudya."

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    41 Yesu wadakhala pafupi ni chombo choikila njhembe panyumba ya Mnungu. Wadaona wandhu umo amachochela njhembe. Wopata ambili adachocha ndalama zambili. 42 Pamenepo wadajha maye mmojhi wafedwa ni mmunake uyo wadali wosauka, wadachocha senti ziwili. 43 Yesu wadaatana oyaluzidwa wake, ni kwaakambila, "Zenedi nikukambilani, maye uyu wosauka wachocha zambili kupitilila onjhe. 44 Wandhu wonjhe achocha ivo vakhalila pachuma chao, nambho maye uyu wafedwa ni mmunake pamojhi ni kusauka kwake wachocha vonjhe walinavo."

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.