43 Yesu anayitana ophunzira ake nati, "Zoonadi, ndikuwuzani kuti mayi wosauka wamasiyeyu waponya zambiri mʼthumbali kuposa ena onsewa. 44 Iwo apereka molingana ndi chuma chawo; koma iye, mwaumphawi wake, wapereka zonse anali nazo ngakhale zoti akanagulira chakudya."
Publicidade
Marko 12:43,44
TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
Em outras traduções
- NTNYBL2025 Nyanja
43 Yesu wadaatana oyaluzidwa wake, ni kwaakambila, "Zenedi nikukambilani, maye uyu wosauka wachocha zambili kupitilila onjhe. 44 Wandhu wonjhe achocha ivo vakhalila pachuma chao, nambho maye uyu wafedwa ni mmunake pamojhi ni kusauka kwake wachocha vonjhe walinavo."
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.