35 Atapita patsogolo pangʼono, anagwa pansi ndi kupemphera kuti ngati ndi kotheka oralo limupitirire. 36 Iye anati, "Abba, Atate, zinthu zonse ndi zotheka ndi Inu. Chotsereni chikhochi. Komabe chitani zimene Inu mukufuna, osati zimene Ine ndikufuna."
Publicidade
Marko 14:35,36
TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
Em outras traduções
- NTNYBL2025 Nyanja
35 Yesu wadapita pachogolo pang’ono, wadajhitaya panjhi chifufumimba, uku ni wapembha, "Ngati ikakhozekana sinidapitila saa iyi ya mavuto." 36 Wadapembha, "Atate wanga, kwanu vindhu vonjhe vikhozekana. Mnichochele chikho ichi cha mavuto, nambho isidakhala ngati umo nifunila ine, nambho ngati umo mfunila imwe."
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.