Pular para o conteúdo
Publicidade

MARKO 15

Imfa ya Yesu

33 Pa ora lachisanu ndi chimodzi masana mdima unabwera pa dziko lonse mpaka pa ora lachisanu ndi chinayi masana. 34 Pa ora lachisanu ndi chinayi Yesu analira mofuwula kuti, "Eloi, Eloi, lama sabakitani?" Kutanthauza kuti, "Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji Ine?"

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também