49 koma atamuona Iye akuyenda pa nyanja, anaganiza kuti anali mzukwa. Iwo anafuwula, 50 pakuti onse anamuona ndipo anachita mantha.
Nthawi yomweyo Iye anawayankhula nati, "Limbani mtima! Ndine. Musachite mantha."