Pular para o conteúdo
Publicidade

Marko 7:10-13

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

10 Pakuti Mose anati, ‘Lemekeza abambo ako ndi amayi ako,’ ndipo, ‘aliyense amene atemberera abambo ake kapena amayi ake ayenera kuphedwa.’ 11 Koma inu mumati, ngati munthu anena kwa abambo ake kapena amayi ake kuti, ‘Thandizo lililonse mukanayenera kulandira kuchokera kwa ine ndi Korobani’ (kutanthauza kuti, mphatso yoperekedwa kwa Mulungu), 12 pamenepo inu simumalola kuti achitire kanthu kalikonse abambo kapena amayi ake. 13 Potero mumachepetsa mawu a Mulungu kukhala wopanda mphamvu ndi miyambo yanu imene mumapatsirana. Ndipo mumachita zinthu zina zambiri monga zimenezi."

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    10 Musa wadaagiza, ‘Alemekeze amako ni atate wako,’ ni ‘Mundhu uyo siwaatukane atate wake kapina amake siwafe.’ 11 Nambho anyiimwe muyaluza ngati mundhu uyo wali ni chindhu chakwaathangatila atate wake ni amake, nambho mkamba, ‘Thandizo ilo nidakupachani ni Kolobani’ mate yake chindhu ichi chapatulidwa ndande ya kumchochela Mnungu, 12 kwakuyaluza chimwecho mwachekeleza wandhu, siwadathangatila atate wao kapina amao. 13 Chimwecho, ndeumo mulidelela mawu la Mnungu ndande ya makhalidwe yanu yayo mudayalandila. Ni mchita vindhu vambili va mtundu umeneo."

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.