Pular para o conteúdo
Publicidade

MARKO 9

28 Yesu atalowa mʼnyumba, ophunzira ake anamufunsa ali pa okha kuti, "Kodi ndi chifukwa chiyani ife sitinathe kutulutsa chiwandacho?"

29 Iye anayankha kuti, "Mtundu uwu umatuluka pokhapokha mwapemphera ndi kusala kudya."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também