Pular para o conteúdo
Publicidade

MALAKI 3

8 "Kodi munthu angathe kuba za Mulungu? Komatu inu mumandibera.

"Koma inu mukufunsa kuti, Kodi timakuberani motani?

"Pa zakhumi ndi pa zopereka. 10 Bweretsani chakhumi chathunthu ku nyumba yosungira, kuti mukhale chakudya mʼnyumba mwanga." Akutero Yehova Wamphamvuzonse, "Tandiyesani, ndipo muone ngati sindidzatsekula zipata zakumwamba, ndi kukugwetserani madalitso ochuluka amene mudzasowe malo owayikamo.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também

Malaquias
Ver todos os capítulos de Malaquias