Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateus 12

Chizindikiro cha Yona

38 Pamenepo ena mwa Afarisi ndi aphunzitsi amalamulo anati kwa Iye, "Aphunzitsi, tikufuna tione chizindikiro chodabwitsa kuchokera kwa Inu."

39 Iye anayankha kuti, "Mʼbado woyipa ndi wachigololo ufunsa za chizindikiro chodabwitsa! Koma ndi chimodzi chomwe sichidzapatsidwa kwa inu kupatula chizindikiro cha mneneri Yona. 40 Pakuti monga Yona anali mʼmimba mwa nsomba yayikulu masiku atatu, usana ndi usiku, momwemonso Mwana wa Munthu adzakhala masiku atatu, usana ndi usiku, mʼkati mwa nthaka.

Veja também