Pular para o conteúdo
Publicidade

MATEYU 13

13 Ichi ndi chifukwa chake ndimayankhula kwa iwo mʼmafanizo:

"Ngakhale akupenya koma saona,

ngakhale akumva koma samvetsetsa kapena kuzindikira.

14 Mwa iwo zimene ananenera Yesaya zikwaniritsidwa:

" Kumva mudzamva koma osamvetsetsa.

Kupenya mudzapenya koma osaona kanthu.

15 Pakuti mtima wa anthu awa ndi wokanika,

mʼmakutu mwawo ndi mogontha,

ndipo atsinzina

kuti asaone kanthu.

Mwina angapenye ndi maso awo,

angamve ndi makutu awo, angamvetse ndi nzeru zawo ndi kutembenuka,

Ineyo nʼkuwachiritsa.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também