25 Pa ora lachinayi usiku, Yesu anabwera kwa iwo akuyendabe pa nyanja. 26 Ophunzira atamuona akuyenda pa nyanja, anaopa nati, "Ndi mzukwa!" Ndipo analira chifukwa cha mantha.
27 Koma Yesu nthawi yomweyo anawawuza kuti, "Limbani mtima! Ndine, musaope."