Pular para o conteúdo
Publicidade

MATEYU 16

15 Iye anafunsa kuti, "Nanga inuyo mumati ndine yani?"

16 Simoni Petro anayankha kuti, "Inu ndinu Khristu, Mwana wa Mulungu wamoyo."

17 Yesu anati kwa iye, "Ndiwe wodala Simoni mwana wa Yona, popeza si munthu amene anakuwululira izi koma Atate anga akumwamba.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também