Pular para o conteúdo
Publicidade

MATEYU 18

28 "Koma wantchito uja atatuluka, anakumana ndi wantchito mnzake amene anakongola kwa iye madinari 100. Anamugwira, nayamba kumukanyanga pa khosi, namuwumiriza nati, Bwezere zimene unakongola kwa ine!

30 "Koma iye anakana. Mʼmalo mwake, anachoka nakamumangitsa kufikira atabweza ngongoleyo.

Veja também