Pular para o conteúdo
Publicidade

MATEYU 19

4 Iye anayankha kuti, "Kodi simunawerenge kuti pachiyambi Mulungu analenga iwo, mwamuna ndi mkazi? 5 Ndipo anati, Pa chifukwa ichi mwamuna adzasiya abambo ake ndi amayi ake nakaphatikana ndi mkazi wake, ndipo awiriwo adzakhala thupi limodzi. 6 Motero salinso awiri ayi koma mmodzi. Nʼchifukwa chake chimene Mulungu wachimanga pamodzi munthu wina asachilekanitse."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também