Pular para o conteúdo
Publicidade

MATEYU 2

5 Ndipo anamuyankha kuti, "Ku Betelehemu wa ku Yudeya chifukwa izi ndi zimene mneneri analemba kuti,

6 " Koma iwe Betelehemu, chigawo cha Yudeya,

sindiwe wamngʼonongʼono mwa olamulira a Yudeya;

pakuti otsogolera adzachokera mwa iwe,

amene adzaweta anthu anga Aisraeli.’ "

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também