Pular para o conteúdo
Publicidade

MATEYU 22

17 Tiwuzeni tsono maganizo anu ndi otani, kodi nʼkololedwa kupereka msonkho kwa Kaisara kapena ayi?"

18 Koma Yesu podziwa maganizo awo oyipa anati, "Inu achiphamaso, bwanji mufuna kundipezera chifukwa? 19 Onetseni ndalama imene mumapereka msonkho." Iwo anabweretsa dinari, 20 ndipo anawafunsa kuti, "Kodi chithunzi ichi ndi malemba awa ndi za ndani?"

21 Iwo anayankha kuti, "Ndi za Kaisara."

Pamenepo anawawuza kuti, "Perekani kwa Kaisara zake za Kaisara, ndi kwa Mulungu zake za Mulungu."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também