Pular para o conteúdo
Publicidade

MATEYU 22

36 "Aphunzitsi, kodi lamulo lalikulu koposa mu malamulo ndi liti?" 37 Yesu anayankha kuti, "Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse ndi moyo wako wonse ndi nzeru zako zonse. 38 Ili ndi lamulo loyamba ndi loposa onse.

Veja também