Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateus 26

Yudasi Avomereza Kupereka Yesu

14 Pamenepo mmodzi wa khumi ndi awiriwo wotchedwa Yudasi Isikarioti anapita kwa akulu a ansembe 15 nafunsa kuti, "Kodi mundipatsa chiyani ngati nditamupereka Iye kwa inu?" Pamenepo anamuwerengera ndalama zokwanira masiliva makumi atatu.

Veja também