Yesu Aneneratu kuti Petro Adzamukana
31 Pamenepo Yesu anawawuza kuti, "Usiku omwe uno inu nonse mudzandithawa, pakuti kwalembedwa:
" ‘Kantha mʼbusa,
ndipo nkhosa zidzabalalika.’
31 Pamenepo Yesu anawawuza kuti, "Usiku omwe uno inu nonse mudzandithawa, pakuti kwalembedwa:
" ‘Kantha mʼbusa,
ndipo nkhosa zidzabalalika.’