Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateus 26

38 Pamenepo anawawuza kuti, "Moyo wanga uli ndi chisoni chofa nacho. Khalani pano ndipo dikirani pamodzi ndi Ine."

39 Atapita patsogolo pangʼono, anagwa pansi chafufumimba napemphera kuti, "Atate anga, ngati ndikotheka, chikho ichi chichotsedwe kwa Ine. Koma osati monga mmene ndifunira, koma monga mufunira Inu."

Veja também