Pular para o conteúdo
Publicidade

MATEYU 27

63 Iwo anati, "Bwana takumbukira kuti munthu wonyenga uja akanali ndi moyo anati, Pakatha masiku atatu ndidzauka.64 Choncho lamulirani kuti manda ake atetezedwe mpaka pa tsiku lachitatu. Chifukwa tikapanda kutero, ophunzira ake angabwere kudzaba mtembo wake ndipo angawuze anthu kuti waukitsidwa kwa akufa. Ndipo chinyengo chomalizachi chidzakhala choyipa kwambiri kusiyana ndi choyamba chija."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também