Pular para o conteúdo
Publicidade

MATEYU 4

Yesu Ayitana Ophunzira ake Oyamba

18 Pamene Yesu ankayenda mʼmbali mwa nyanja ya Galileya, anaona abale awiri, Simoni wotchedwa Petro ndi mʼbale wake Andreya akuponya khoka mʼnyanja popeza anali asodzi. 19 Yesu anati, "Bwerani, tsateni Ine ndipo ndidzakusandutsani asodzi a anthu."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também