Pular para o conteúdo
Publicidade

MATEYU 5

Mchere ndi Kuwunika

13 "Inu ndinu mchere wa dziko lapansi. Koma ngati mcherewo usukuluka, adzawukometsanso ndi chiyani? Ulibenso ntchito koma kungowutaya kunja, anthu nawuponda.

14 "Inu ndinu kuwunika kwa dziko lapansi. Mzinda wa pa phiri sungathe kubisika.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também