Publicidade

Mateus 5

Zokhudza Chigololo

27 "Munamva kuti kunanenedwa kuti, Usachite chigololo. 28 Koma Ine ndikuwuzani kuti aliyense woyangʼana mkazi momusirira wachita naye kale chigololo mu mtima mwake.

Veja também

Publicidade
Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-06-29_22-07-56-