Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateyu 6:31-34

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

31 Chifukwa chake musadere nkhawa ndi kuti, ‘Tidzadya chiyani?’ kapena ‘Tidzamwa chiyani?’ kapena ‘Tidzavala chiyani?’ 32 Pakuti anthu akunja amazifuna zinthu zonsezi ndipo Atate anu akumwamba adziwa kuti musowa zimenezi. 33 Koma muyambe mwafuna ufumu wake ndi chilungamo chake ndipo zinthu zonsezi zidzapatsidwa kwa inu. 34 Chifukwa chake musadere nkhawa ndi za mawa, popeza tsiku lililonse lili ndi zovuta zake zokwanira.

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    31 "Chimwecho, msadajhichaucha nimkamba, ‘Sitidye chiyani! Kapina sitimwe chiyani! Kapina sitivale chiyani!’ 32 Pakuti yameneyo yonjhe wandhu yao siamjhiwa Mnungu ajhichauchila yaya yonjhe. Atate wanu akumwamba ajhiwa kuti mfuna ivi vonjhe. 33 Chimwecho, ufuneni uti ufumu wa Mnungu ni kuchita yayo wayafuna Mnungu, ni iye siwakupacheni yaya yonjhe. 34 Ndiipo, msadajhichauchila ya mawa, pakuti mawa siijhichauchile yeneyake. Kila siku lijhichauchila lene lake."

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.