Pular para o conteúdo
Publicidade

MATEYU 8

2 Ndipo munthu wakhate anadza kwa Yesu namugwadira nati, "Ambuye, ngati mufuna, mukhoza kundiyeretsa."

3 Yesu anatambasula dzanja lake namukhudza munthuyo nati, "Ndikufuna, yeretsedwa!" Nthawi yomweyo anachiritsidwa khate lake. 4 Ndipo Yesu anati kwa iye, "Taona, usawuze wina aliyense. Koma upite kwa mkulu wa ansembe ukadzionetse wekha ndi kupereka mphatso imene Mose analamulira, kuti ukhale umboni kwa iwo."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também