Pular para o conteúdo
Publicidade

Nehemiya 13:10-12

10 Ndinapezanso kuti Alevi sankalandira magawo awo amene amayera kulandira. Chotsatira chake Alevi onse pamodzi ndi oyimba nyimbo amene ankagwira ku Nyumba ya Mulungu anathawa, aliyense kupita ku munda wake. 11 Choncho ndinadzudzula akuluakulu aja ndipo ndinawafunsa kuti, "Nʼchifukwa chiyani Nyumba ya Mulungu yasiyidwa?" Ndipo ine ndinawayitanitsa pamodzi ndi kuwayika mʼmalo awo.

12 Pambuyo pake Ayuda anayambanso kubwera ndi zopereka zawo za chakhumi cha tirigu, vinyo ndi mafuta kuti ziperekedwe ku nyumba yosungiramo chuma.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.