Pular para o conteúdo
Publicidade

NUMERI 13

31 Koma anthu aja amene anapita naye anati, "Sitingathe kulimbana ndi anthuwo popeza ndi amphamvu kuposa ifeyo." 32 Choncho anthuwo anafalitsa pakati pa Aisraeli mbiri yoyipa ya dziko lomwe anakalionalo. Iwo anati, "Dziko limene tinapita kukalizonda limawononga anthu okhala mʼmenemo. Ndipo anthu onse amene tinakawaona kumeneko ndi ataliatali. 33 Kumeneko tinaona Anefili (ana a Aanaki ochokera kwa Nefili). Ifeyo timangodziona ngati ziwala mʼmaso mwawo, ndipo kwa iwo timaonekadi motero ndithu."

Veja também