Pular para o conteúdo
Publicidade

AROMA 12

19 Okondedwa anga, musabwezere choyipa, koma lekerani Mulungu. Pakuti kwalembedwa, "Kubwezera chilango nʼkwanga. Ndidzawalanga ndine," akutero Ambuye. 20 Koma,

"Ngati mdani wako ali ndi njala, mupatse chakudya.

Ngati ali ndi ludzu, mupatse kanthu kakumwa.

Pochita ichi, udzamuwunjikira makala amoto pamutu pake."

21 Musagonjetsedwe ndi choyipa, koma gonjetsani choyipa pochita chabwino.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também