Pular para o conteúdo
Publicidade

Aroma 13:1-3

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

Kumvera Aulamuliro

1 Aliyense ayenera kumvera akulu olamulira, chifukwa palibe ulamuliro umene sunachokere kwa Mulungu. Olamulira amene alipo anayikidwa ndi Mulungu. 2 Kotero kuti, iwo amene awukira ulamuliro atsutsana ndi chimene Mulungu anakhazikitsa. Ndipo amene atero adzibweretsera okha chilango. 3 Pakuti olamulira saopseza amene amachita zabwino koma amene amachita zoyipa. Kodi mukufuna kukhala osaopa olamulira? Tsono chitani zoyenera ndipo adzakuyamikirani.

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    1 Kila mundhu wafunika kwavela yawo ali ni ulamulilo aselikali, pakuti alamuli wonjhe achokela kwa Mnungu, ni anyiiwo ali ni ulamulilo aikidwa ni Mnungu 2 Uyo waachucha yawo ali ni ulamulilo waachucha lamulo la Mnungu, ni anyiawo achita chimwecho salamulidwe achinawene. 3 Pakuti alamuli sapeleka mandha kwa wandhu yawo achita vabwino, nambho apeleka mandha kwa wandhu yao achita voipa. Chipano ufuna siudamwopa mundhu uyo wali ni ulamulilo? Chita vabwino niiwe siwakuelekele.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.