Pular para o conteúdo
Publicidade

Aroma 14:13,15,17

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

13 Motero, tiyeni tisiye kuweruzana wina ndi mnzake. Mʼmalo mwake, tsimikizani mʼmaganizo anu kuti musayike chokhumudwitsa kapena chotchinga mʼnjira ya mʼbale wanu. 15 Ngati mʼbale wako akuvutika chifukwa cha chimene umadya, iwe sukuchitanso mwachikondi. Usamuwononge mʼbale wako amene Khristu anamufera chifukwa cha chakudya chakocho. 17 Pakuti Ufumu wa Mulungu si nkhani yakudya ndi kumwa, koma chilungamo, mtendere ndi chimwemwe mwa Mzimu Woyera.

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    13 Chipano tisiye kwalamula okhulupilila anjathu, nambho tilamule kuti tisiye kuchita chalichonjhe icho sichimchitiche okhulupilila mnjathu wachite machimo. 15 Ngati ukamdandaulicha mbale wako ndande ya chakudya icho ukudya, basi siuchogozedwa ni chikondi. Siudavomela ata pang’ono chakudya chako chikhale ndande ya kutaika kwa mundhu mwina uyo Kilisito wadamwalila ndande yake. 17 Pakuti ufumu wa Mnungu osati kudya ni kumwa, nambho ni kukahala ukhalo uwo umkhwadilicha Mnungu, mtendele ni kukondwela uko kupelekedwa ni mzimu wa Mnuungu.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.