Pular para o conteúdo
Publicidade

Romanos 6

20 Pomwe munali akapolo atchimo, simunkalabadira za chilungamo. 22 Koma tsopano pakuti inu mwamasulidwa ku tchimo ndipo mwasanduka akapolo a Mulungu, phindu lomwe mulipeza ndi kuyera mtima ndipo chotsatira chake ndi moyo wosatha.

Veja também