Pular para o conteúdo
Publicidade

AROMA 8

15 Mzimu amene inu munalandira samakusandutsani akapolo, kuti muzikhalanso amantha, koma Mzimu amakusandutsani ana. Ndipo mwa Iye ife timafuwula kuti, "Abba, Atate." 16 Mzimu mwini amavomerezana ndi mzimu wathu kuti ife ndife ana a Mulungu.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também