Pular para o conteúdo
Publicidade

Romanos 8

35 Ndani amene adzatilekanitsa ife ndi chikondi cha Khristu? Kodi ndi masautso, kapena zowawa, kapena mazunzo, kapena njala, kapena umaliseche, kapena choopsa, kapena lupanga? 36 Monga kwalembedwa:

"Chifukwa cha inu, ife tikuphedwa tsiku lonse:

ife tikutengedwa ngati nkhosa zoti zikaphedwe."

37 Ayi, mu zonsezi ife ndife oposa agonjetsi mwa Iye amene anatikonda.

Veja também