Pular para o conteúdo
Publicidade

YAKOBO 1

5 Ngati wina pakati panu akusowa nzeru, apemphe kwa Mulungu amene amapereka kwa onse mwaulere ndi mosatonzera, ndipo adzapatsidwa. 6 Koma pamene mupempha, muyenera kukhulupirira osakayika, chifukwa amene amakayika ali ngati mafunde pa nyanja amene amawinduka nakankhika ndi mphepo. 7 Munthu wotere asayembekezere kulandira kalikonse kuchokera kwa Ambuye. 8 Iyeyu ndi munthu wa mitima iwiri, wosakhazikika pa zimene akuchita.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também