12 Koposa zonse, abale anga, musamalumbire. Polumbira osamatchula kumwamba kapena dziko lapansi, kapena china chilichonse. "Inde" wanu azikhala "Inde," ndipo "Ayi" wanu azikhala "Ayi," kuopa kuti mungadzapezeke olakwa.
Publicidade

+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.