Maria
Maria, mãe de Jesus, é honrada nas Escrituras como a mulher escolhida por Deus para trazer ao mundo o Salvador. Sua fé, humildade e obediência são exemplo para todos os cristãos.
A escolhida de Deus
O anjo Gabriel anunciou a Maria que ela seria mãe do Filho do Altíssimo. Ela respondeu com fé: 'Faça-se em mim segundo a tua palavra.'
Kubadwa kwa Yesu kuuzilidwa
Mumwezi wa sita wa pathupi pa Elizabeti, Mnungu wadamtuma mtumiki wake Gabilieli kupita kumujhi wa Galilaya, uwo utanidwa Nazaleti, wapite kwa mwalimbeta uyo wamatanidwa Maliya, uyo wadapachidwa chilipa ni wammuna uyo wamatanidwa Yusufu, wa mbadwa wa Daudi. Mtumiki wa kumwamba wa Mnungu wadamchokela ni kumlonjela ni kumkambila, "Iwe wapachidwa mwawi, Ambuye ali pamojhi ni iwe!"
Nambho mtumiki wa kumwamba wa Mnungu wadamkambila, "Maliya usadaopa, pakuti Mnungu wakupacha mwawi. Vechela, siupate pathupi ni kubala mwana wa mmuna, niiwe siumpache jhina Yesu. Iye siwakhale mundhu waulamulilo, ni siwatanidwe mwana wa Uyo wali kumwamba kupunda. Ni Ambuye Mnungu sampache ufumu ngati umo wadali Daudi, tate wake. Chimwecho iye siwalamulile mbadwa wa Yakobo muyaya, ni ufumu wake siukhala ni mathelo!"
Kubadwa kwa Yesu Kilisito
Kubadwa kwa Yesu Kilisito kudali chimwechi. Maliya maye wa Yesu wadachumbidwa ni Yusufu. Nambho akali osakhale pamojhi ngati mundhu ni mkazake, Maliya wadaonekana wali ni pathupi kwa mbhavu za Mzimu Woyela.
O Magnificat
Maria cantou: 'Minha alma engrandece ao Senhor!' Seu cântico exalta a misericórdia, o poder e a fidelidade de Deus.
Maliya waimba kumkweza Mnungu
Maliya wadakamba,
"Mtima wanga umkweza Ambuye,
ni mtima wanga ukondwela ndande ya Mnungu Muomboli wanga.
Pakuti Mnungu wanikumbukila kwa lisungu ine mbowa wake wojhichicha. Kuyambila chipano mibadwa yonjhe siinitane wamwawi.
Pakuti Mnungu wambhavu zonjhe wanichitila vavikulu,
jhina lake ni woyela.
Lisungu lake kwa anyiyawo amulemekeza kupunda
ni lolimba kwa mibadwa ni mibadwa.
iye wachita vindhu vavikulu kwa mbhavu zake,
wayamwaza maganizo ya wandhu ambwinya yayo yali mmitima yawo,
iye waachicha alamuli kuchokela mmipando yawo ya chifumu,
nambho waakweza yawo ajhichicha.
Anjala wakhuticha vindhu vabwino,
ni wandhu wopata watopola manja yachajhe.
Iye wamthangatila Izilaeli mbowa wake,
ni wakumbukila ahadi yake yomlengela lisungu,
ngati umo wadakambila kwa anyambuyathu,
Ibulahimu ni mibadwa yake yonjhe muyaya."
Yusufu wadachoka kumujhi wa ku Nazaleti uwo uli mujhiko la ku galilaya, wadapita kumujhi wa Beselehemu uwo uli kujhiko la Yudea, uko wadabadwila mfumu Daudi. Yusufu wadapita kumeneko ndande iye wadali wa mbadwa wa mfumu Daudi. Iye wadapita kuwelengedwa pamojhi ni Maliya, uyo wadampacha chilipa, nayo wadali ni pathupi. Yapo adali kumeneko ku Beselehemu, ndhawi yojhipenyelela Maliya idakwanila, ni wadajhimasula mwana wake wachisamba, wammuna. Iye wadamvinikila matewela ni kumgoneka mchidiku chasependwa ndande yodyechela ng’ombe, chifuko anyiiwo siadapate malo mnyumba ya alendo.
Nambho Maliya wadaganizila ni kuyasunga mawu yajha mumtima mwake.
Simiyoni wadaapacha mwawi, ni kumkambila Maliya make wa mwana, "Mwana uyu siwakhale chifuko cha khugwa ni kuomboka wandhu ambili mu Izilaeli. Iye siwakhale chizindikilo chochokela kwa Mnungu icho sichikanidwe ni wandhu ambili, ni maganizo ya wandhu ambili siyaonekane padanga, ni iwe umwene wake siudandaule kupunda."
Wobala wake yapo adamuona adazizwa kupunda. Maliya, make wamwanayo wadamfunjha, "Mwana wanga, ndande yanji watichitila chimwechi? Atate wako ni ine timakufunafuna tali ni mandha." Iye wadaafunjha, "Ndande yanji mnifunafuna ine? Bwanji, simujhiwa kuti ine nifunika kukhalapo panyumba ya atate wanga?" Nambho wobala wake siadajhiwe mate ya mawu yayo wadakambila mwana wao.
Ndiipo Yesu wadabwela pamojhi ni anyiiwo mbaka ku Nazaleti, iye wamavela. Nambho amake adavisunga vindhu vonjhe mumtima.
Mãe fiel até o fim
Maria acompanhou Jesus desde o nascimento até a cruz. Ela estava entre os discípulos no Pentecostes, fiel em oração.
Divai yapo idatha, amaye wake adamkambila Yesu, "Divai yatha."
Ndiipo Yesu wadayangha amaye wake, "Ndandeyanji munikambila nghani imeneyo. Ndhawi yochita njhito yanga ikali yosafika."
Chimwecho amake adazikambila mbowa, "Chilichonjhe icho siwakukambileni, chitani,"
Pafupi ni mtanda wa Yesu adaima amaye wake, akulu wao wa amake, Malia wamkazi wa Kileopa, ni Malia uyo wadachokela kumujhi wa Magidala. Yesu yapo wadaona amake aima pafupi ni oyaluzidwa uyo wamamkonda, wadaakambila amaye wake, "Maye! Mwana wanu uyo yapo."
Ndiipo wadamkambila yujha oyaluzidwa wake Yohana, "Amaye wako yawo yapo." Kuyambila ndhawi imeneyo oyaluzidwayo wadatengedwa ni amaye wake Ayesu kukhala kukhomo kwao.
Achaabale auzene a Yesu
Amake ni achabale wake Yesu adafika pamenepo, adaima kubwalo, adamtuma mundhu mkati kuti wakamtane Yesu. Gulu la wandhu lidamzungulila Yesu. Nawo wandhu wajha adamzungulila adamkambila, "Amako ni achabale wako ali kubwalo, atokufuna iwe." Yesu wadaafunjha, "Maye wanga ni achabale wanga ni achiyani?" Pamenepo wadaapenya wandhu wajha adamzungulila ni kukamba, "Penyani, anyiyawa nde maye wanga ni achabale wanga auzene. Mundhu waliwonjhe uyo wachita yayo wayafuna Mnungu, mmeneyo nde mkulu wanga ni mlongowanga ni maye wanga."
Bwanji, uyu opande mwana wa osepa mitengo yokonjela vindhu? Bwanji, maye wake osati Maliya? Bwanji, abale wake osati Yakobo, Yosufu, Simoni ni Yuda? Bwanji, ni achabale wake, siali pamojhi ni ife pano? Bwanji wapata kuti yaya yonjhe?"
Anyiyawa wonjhe adaendekela kupezana pamojhi kupembhela. Pakati pawo padali ni Maliya maye wake wa Yesu ni waachikazi wina, ni pamojhi ni achabale wake a Yesu.