12Pampajha, Mzimu Woyela udamchogoza Yesu kupita kuphululu,
15Wadakamba, "Nyengo ya Mnungu yakwana yolamulila wandhu. Lapani ni kukhulupilila Uthenga Wabwino."
26Chiwanda chimenecho chidamtingiza kwa mbhavu mundhu yujha, chidalila kwa mvekelo waukulu, ni kumchoka.