Pular para o conteúdo
Publicidade

1 AKORINTO 15

54 Pamene thupi lovundali likadzasanduka losavunda, ndipo thupi lotha kufali likadzasanduka losatha kufa, pamenepo zidzakwaniritsidwa zimene zinalembedwa zakuti, "Imfa yogonjetsedwa kwathunthu."

55 "Iwe imfa, kupambana kwako kuli kuti?

Iwe imfa, ululu wako uli kuti?"

56 Ululu wa imfa ndi tchimo, ndipo mphamvu ya tchimo ndi lamulo. 57 Koma tiyamike Mulungu amene amatipambanitsa mwa Ambuye athu Yesu Khristu.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também